MTENDERE

Reads: 906  | Likes: 1  | Shelves: 1  | Comments: 0

More Details
Status: Finished  |  Genre: Romance  |  House: solo series
Atachitidwa chipongwe ali mwana, Solobala adakhala ndi nkhwidzi zodadzabwenzera. Iye adaona kut ndi njira yokhayo yomwe akadatha kupeza mtendere.
***
Mbali inayi, twin-sister wake, Solofina adali akuganiza kut adzapeza mtendere akadzakhala mchikondi... Mwamwai kay mwa tsoka, ana awiriwa omwe adakulira kosiyana, adakumana koma samadziwana... Zinthu zidavuta poti awiriwa amaumva mtendere mosiyana...
***
Nkhaniyi ikukamba za mtendere; 1+Momwe ena amaumvetsetsera... 2+Momwe ena amausakira... 3+Momwe kusakakwamtendere kukhoza kuonjezera mavuto komanso 4+ Mtendere weniweni... To God be the Glory!

Table of Contents

Chiyambi

Submitted: June 27, 2016

"TAIMA POMPO IWE!" uyu anali Solofina kumuuza msungwana wantchito wakwao yemwe anali akusesa panja. Msungwanayu, dzina lake Alinafe, anal... Read Chapter

Solofina zimuonekera...

Submitted: June 27, 2016

Fina adayamba kucheza ndi Chiso yemwe adapezeka kut adali wammuna. Kaya ndi chani koma mnyamatayu adapezeka kut adali wophunzira wakusuku... Read Chapter

Solofina abalalika...

Submitted: June 27, 2016

"A GELO, ZIKUKHALA BWANJI APA?? GALIMOTO YANGAYI MUKUTANI NAYO APA??" uyu anali Fina kumuphamika Nafe ndimafunso. Nafe ankangomwetulira k... Read Chapter

Umbeta wamuthera Solofina??

Submitted: June 27, 2016

Fina anapita kuchipinda kwake komwe anangofikira pa laptop ndikulowa pa facebook. Anapeza kuti Chisomo sali pa line nde anangolemba uthen... Read Chapter

Gift+Nafe....Chiso+Fina

Submitted: June 27, 2016

"Aah Chisomo ndi iweyo?? haha nde ku party kuja sumanena bwanji??" adafunsa Fina chimwemwe chili khathikhathi pa kankhope yake yonse. "Mm... Read Chapter

Gift nd Nafe....

Submitted: June 27, 2016

.Mmene Alinafe amafika kunyumba, naye Solofina anali akutulukira. Chomwe chinamudabwitsaNafe chinali choti Fina ankangomwetulira.. "Eeh e... Read Chapter

Solofina agwa mchikond??

Submitted: June 27, 2016

Mawa lake ataweruka ku sukulu, anapita ku Soche kukakumana ndi Chiso. Uku anapeza kuli socials ndipo anadziwa kuti mwina Chisomo atasanga... Read Chapter

Solofina wapez ka mtetezi kake??

Submitted: June 27, 2016

Chiso anaoneka wankhawa kwabasi ndipo anamupepesa Fina yemwe anati palibe cholakwika. Chiso anamuuza Fina kuti sizimayenera kutero poti a... Read Chapter

Solofina...

Submitted: June 28, 2016

"Chabwino tavula magalasi ndi chipewachi kuti ndikuone nkhope pleeeeaaaasssse!" Fina anachondelera.."Mayazi...Sukuyenera kutero. Chomwe n... Read Chapter

Chinsinsi kodi??

Submitted: June 28, 2016

"Mmm Ma, paja ndili ndi zaka 23... Nde kuba akabe ineyo??" anayankha Fina mumtima akuvomerezana nawo mai ake. Anadziwa kuti atawafotokoze... Read Chapter

Abambo taululani pulizi!

Submitted: June 28, 2016

Kwa thawi yoyamba, bambo ake anamulondola ndikukamupepesa. Fina anadabwa ndikusintha kwa abambo ake'ku.+ *xxxx*xxxx*Mawa kutacha, Fina an... Read Chapter

Kufuna kudziwa...

Submitted: June 28, 2016

Fina asanayankhe, kunabwera mlonda yemwe anamuuza Fina kuti kwabwera mnyamata yemwe amamufuna.Bambo anamuuza mlondayu kut amuuze mnyamata... Read Chapter

Chiso kwa Fina...

Submitted: June 28, 2016

."Mm muli bwanji bambo??" Chiso anapereka moni pofuna kudula nkhani. Bambo anaitulukira ndipo anatsanzika ndikunyamuka."Daddie, kodi simu... Read Chapter

Nkhani yangoyambika apa!

Submitted: June 28, 2016

."Ukati poti umandikonda ukutanthauza chani??" Fina anafuna kudziwa.."Kunena mosabisa, ndiwe mamuna alilenji; ndiwe wokongola, wakhalidwe... Read Chapter