MTENDERE

Reads: 1239  | Likes: 1  | Shelves: 1  | Comments: 0

More Details
Status: Finished  |  Genre: Romance  |  House: solo series

Chapter 14 (v.1) - Nkhani yangoyambika apa!

Submitted: June 28, 2016

Reads: 117

A A A | A A A

Submitted: June 28, 2016

A A A

A A A

."Ukati poti umandikonda ukutanthauza chani??" Fina anafuna kudziwa.."Kunena mosabisa, ndiwe mamuna alilenji; ndiwe wokongola, wakhalidwe, komanso wochezeka. Ndimafuna kugwa nawe mchikondi komabe ndimakhala ndi mantha." adatero Chiso akuseweretsa mabatani a shirt yake.."Ndinakuuza ungochotsa mantha!" Fina adamukumbutsa Chiso uku akumugwira manja. Chiso anamuyang'ana Fina mooneka kuti wakopeka. Fina anamwetulira mumtima kuti tsopano zikuyenda."Nde tanena ukutipo bwanji Chiso??" Fina adafunsa ndikankhope kachisoni."Okay! Khfufkhfu!" Anakhosomola mwachifuwa. "Fina...Ndako... aaaa iwe!" mau ake adathera panjira pomwe anamuona Nafe. "Fina, ndi Alinafe uyo et??" Anafunsa akuloza Alinafe yemwe anali atasintha njira.."Eya. Watani?? Ukumudziwa??" Fina anafunsa mtima wake uli mmwamba poti amayembekezera kuthetsa umbeta wake.."Aaa noo! Ungamuitaneko??" Chiso anafunsa akuonetsa kuti wabalalikiratu.Fina samamvetsa komabe anamuitana Nafe kuti mwina zikhoza kuululika..........The story continues...Wait for book 2....


© Copyright 2019 Chiyamiko isobar chiusiwa. All rights reserved.

Chapters

Add Your Comments: