Zokonza kale

Reads: 1695  | Likes: 0  | Shelves: 0  | Comments: 0

More Details
Status: In Progress  |  Genre: Romance  |  House: solo series
Kukumana kwa Janet ndi Chrispin kudali kodabwitsa ndipo kudasinrtha zinthu zambiri m'banja mwa kwa Chris...Ma udani komanso zitokotoko.

Table of Contents

Chrispin

Submitted: July 03, 2016

"MWAKULA INU MUKWATIRE AAAAHHH!!" awa adali mai a Chrispin kumulangiza mwana wao yemwe amaoneka kut za banja zimamutalikira. Mai akewa nk... Read Chapter

amai akufuna mpongozi

Submitted: July 03, 2016

Mai adapanga ka tea ndipo nkhani zidabulika. Mkat mwa nkhanizi, mai amakonda kufunsa nkhani zokwatirakwatira zomwe zimamunyasa Chris. Mba... Read Chapter

Msungwana wachilendo...

Submitted: July 03, 2016

Mai adamunyamula msungwanayu ndkulowa naye mnyumba ali chigonere. Atangomunyamula, Chris adafulumira kukwera galimoto ndikunyamuka... ***... Read Chapter

Chris ndi Tsegho...Mphaka ndi khoswe

Submitted: July 03, 2016

Iwo adamuona kut amafuna kuwauza chinachake koma ankalephera. Posafuna kumubalalitsa, adangokhala ngat sadaone kalikonse. Onse adakhala p... Read Chapter

Chris ndi Goodson amenyanairana Tsegho...

Submitted: July 03, 2016

Mai adamupatsa kampando kut akhalire pakapinga ndipo adamubweretseranso ka Fanta kut azitsitsira akumudikira Chris. Iye adawathokoza ndip... Read Chapter

Chris ali ndi mkazi??

Submitted: July 03, 2016

Iye adawayang'an kenako adayang'ana mmwamba atapisira mmatumba, "amami, kulibwino kut ndisakuyankheni. Mwina h*le lanu mukulisungalo ndil... Read Chapter

Goodson akulowa mkat...

Submitted: July 04, 2016

Msungwanayu adamupepesa Chris yemwe adangotsonya ndikupit aku chipind kwake. Atangochoka, Tsego adaseka ndipo adadziyankhulira, "Apapa Mi... Read Chapter

Goodson samala!

Submitted: July 05, 2016

Tsegho adamutembenukira Godson kenako adaseka, "Haha! Wafunsiranj??" adafunsa Tsegho ndipo Goodson adapanga manyazi, "Basi...Kungot ukuon... Read Chapter

Chris akamba zakukhosi...

Submitted: July 05, 2016

Usiku, onse adamudikira Chris kut adzadyere limodzi... Chris atafika, tebulo lidayalidwa kenako adamuitanira kut adzadye limodzi. Iye ada... Read Chapter

Mayesero...

Submitted: July 05, 2016

Mai ake adamuuza kut amutaye kaye koma iye adakana ponena kut adali mchikondi ndi mkazi wapa Facebook'yo basi...Mmene awiriwa amakambiran... Read Chapter

Chris wayambba kugodoka??

Submitted: July 05, 2016

Tsegho adaseka kenako adamuuza Chris kut agone bwino... Sabata imeneyi mai adali osangalala kwambiri pot Chris amacheza kwambiri ndi Tseg... Read Chapter

Linda tsopano...

Submitted: July 06, 2016

Chris adakhulupirira ndipo adadekhetsa mtima ndikumusiya mlonda uja. Iye adabwerera pa tebulo pake ndikukapitirizakucheza ndi Tsegho koma... Read Chapter

tsegho waopsa...

Submitted: July 06, 2016

"Goo...Good...Goodson! Aaah!" adangotero akulira. Tsegho adatsika kut akaone zomwe zimachitikazo ndipo adafikira kumufunsa Chris chomwe c... Read Chapter

Bambo a Tsegho!!

Submitted: July 06, 2016

Chris ataona kut Tsegho amachedwa pa phone'po, adamulondola ndipo adangomva nawo mau akumamaliziro, "Ee mukhoza kubwera mawa bye!" adater... Read Chapter

Tsegho adziulula yekha ndi zolinga zake...

Submitted: July 06, 2016

"OOOOOOH LOOK AT HER...THE MOST COURAGEOUS DAUGHTER (Msungwana wolimba mtima kwabasi.)!" adatero ndipo Tsegho naye adawayankha mchizungu ... Read Chapter

Amai auma mtima...

Submitted: July 06, 2016

"Ndikudziwa umandikonda...Ndikudziwa Mai akonso omuwakonda...Ndikudziwa ndiwe womvera komansi Chris amene ndimamudziwa ineyo ndi wopirira... Read Chapter