Reads: 193

"Ndikudziwa umandikonda...Ndikudziwa Mai akonso omuwakonda...Ndikudziwa ndiwe womvera komansi Chris amene ndimamudziwa ineyo ndi wopirira. Okay, pita kwa mai ako ndipo ineyo ndi nyamuka ndi bambo anga koma udziwe kut sindisiya kukukonda. Tingodikira mtima wa mai ako uphwee kaye..." adatero akumuyang'ana Chris mmaso kenako adamukissa ndikupita pomwe padali ama aja, "Mamie, mwakhala nat kholo kwa ine ndipo sindidzaiwala chimenechi. Zimakhala zovuta kumakubisirani komabe munkathandizira mission nde sindikadakuuzani. Munkamuletsa kuganizira za 'ine' wa pa fb yet mukumukankhira mwana wanu kwa 'ine' wapakhomo...Chonde mundikhululukire!" adapepesa Janet koma sadayankhidwe. Iye adanyamuka ndi bambo ake nkumauyamba wopita kwao komwe kudali pafupifupi ma kilometer 10 kuchoka kwa Chris'ku. ... Chris adamwetulira ndikuwauza amai ake kut amamukonda Janet koma iw adat sangalore kukhala ndi munthu wa bodza ngat Janet. Inde! Iwo adali atasweka mtima zenizeni.


Submitted: July 07, 2016

© Copyright 2021 Chiyamiko isobar chiusiwa. All rights reserved.

Chapters

  • Facebook
  • Twitter
  • Reddit
  • Pinterest
  • Invite

Add Your Comments:


Facebook Comments

Other Content by Chiyamiko isobar chiusiwa

Book / Mystery and Crime

Short Story / Mystery and Crime