MADZI AKATAIKA

Reads: 2380  | Likes: 0  | Shelves: 0  | Comments: 0

More Details
Status: In Progress  |  Genre: Romance  |  House: solo series
Asungwana awiri anachimwitsidwa ndi mnyamata mmodzi ndipo ana awo anabadwa tsiku limodzi...
Nkhani yomwe idavuta idali yot mnyamatayu akwatira ndan...
Mavuto awowa adaululitsa zinsinsi zakalekale za makolo aanawa ndipo zinthu zidavuta kwabasi...

Table of Contents

Atengambali...

Submitted: July 08, 2016

."KOD UMANDIFUNA ETI?? KOMA IWE UDZAKHUZUMUKA LITI??" uyu adali Emily kundilalatira pomwe ndinamupempha kut ndikhale nawo pa tebulo limen... Read Chapter

Solo akumufookera Lerato...

Submitted: July 08, 2016

"SOLO UMANDICHITIRA MANYAZI BWANJ?? TIZITI SINDIMAKUYENERA??" adafunsa msungwanayu akundiyandikira. Millias anaseka koma akuoneka odabwa,... Read Chapter

Solo achitidwa chipongwe...

Submitted: July 08, 2016

Episode imeneyi ndi yomwe pagona nkhani nde ndiyofunika kuimvetsa komanso kuikumbukira bwino... Read Chapter

Solo akadali ndi chikondi pa Lerato??

Submitted: July 08, 2016

"TATULUKA MNYUMBA MWANGA MUNO MWACHANGU!" Anamukuwira mphaka yemwe adali atalowera pa window. Emily adamuthamangitsa mphaka uja kenako ad... Read Chapter

Lerato ndi wokupha??

Submitted: July 09, 2016

Lerato amangidwa poganiziridwa mlandu wakupha...Solo wabalalika ndipo alandira uthenga wina wobalalitsa... Read Chapter

Solo wachimwitsa mkazi...

Submitted: July 09, 2016

Solo wachimwitsa Emily ngakhale kut akukaikira. Mai ake atamva izi amuthamangitsa. Bambo a Emily avomera kumutenga koma ati akwatirane ndi Emily...

Lerato ali kundende Read Chapter

"Solo, koma wapangachi ndichiganizo chabwino??"

Submitted: July 09, 2016

Emily wakwaniritsa khumbo lake...
Read Chapter

kwabadwa mapasa...

Submitted: July 12, 2016

"KODI MA HUG SACHITIKA APA?? AAAA KOMA ALICIA!" adafunsa Emily ndipo tonse tinaseka. Iye anamuhaga Billiat ndipo ine ndinamuhaga Alicia. ... Read Chapter

kwabadwa mapasa...

Submitted: July 12, 2016

."TAIMA POMPO!" Galimoto lija linaima ku malo akutali kufupi ndi phiri la Soche ndipo ananditulutsa mu galimoto ija. Anthuwa anali ataval... Read Chapter

kwabadwa mapasa...

Submitted: July 12, 2016

MADZI AKATAIKA SAOLEKA!!!! Read Chapter

kwabadwa mapasa...

Submitted: July 12, 2016

"SOLO, UKUTI LERATO NDI MNG'ONO WANGA?? OOOH! NO! ZOONA NDINAOMBERA MNG'ONO WANGA???" anafunsa Emily asakukhulupirira. Ndinaona misozi ik... Read Chapter

Zikunka ziipiraipira...

Submitted: July 12, 2016

Kodi mai anga ndi Emily amagwirizana chani
chimene chawapangitsa kuima mutu chonchi??
Kodi ine Solo ndapanga chinthu chabwino posamala
za Emily ndikusalabada za Lerato??
Mutakhala Lerato mungamukhululukire Emily??
Read Chapter