Kamuzumalawi stories, books, poems, and more

6 results

A brave youngman, Solo, is on a mission to avenge his mothers death by seeking justice. However, the deeper he goes, the tougher it gets as people close to him were part of the injustice,,, patiently follow the story to see what's more valuable to Solo; ustice or family... Read More

Asungwana awiri anachimwitsidwa ndi mnyamata mmodzi ndipo ana awo anabadwa tsiku limodzi... Nkhani yomwe idavuta idali yot mnyamatayu akwatira ndan... Mavuto awowa adaululitsa zinsinsi zakalekale za makolo aanawa ndipo zinthu zidavuta kwabasi... Read More
Kukumana kwa Janet ndi Chrispin kudali kodabwitsa ndipo kudasinrtha zinthu zambiri m'banja mwa kwa Chris...Ma udani komanso zitokotoko. Read More

Reads: 1244

Shelves: 1

The solo series House

Atachitidwa chipongwe ali mwana, Solobala adakhala ndi nkhwidzi zodadzabwenzera. Iye adaona kut ndi njira yokhayo yomwe akadatha kupeza mtendere. *** Mbali inayi, twin-sister wake, Solofina adali akuganiza kut adzapeza mtendere akadzakhala mchikondi... Mwamwai kay mwa tsoka, ana awiriwa omwe adakulira kosiyana, adakumana koma samadziwana... Zinthu zidavuta poti awiriwa amaumva mtendere… Read More
Am just trying to introduce the main characters... Read More
Tickle My Funny Bone Comedy Writing Contest 2018

Welcome New Writers